Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 13:38, 39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Tsopano dziwani abale anga kuti, ife tikulalikira kwa inu za kukhululukidwa kwa machimo kudzera mwa ameneyu.+ 39 Dziwaninso kuti pa zinthu zonse zimene kunali kosatheka kuti muonedwe opanda mlandu kudzera mʼChilamulo cha Mose,+ aliyense wokhulupirira akuonedwa wopanda mlandu kudzera mwa iyeyu.+

  • Agalatiya 2:15, 16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ifeyo amene ndi a mtundu wa Chiyuda, osati ochimwa ochokera mwa anthu a mitundu ina, 16 tikudziwa kuti munthu amaonedwa kuti ndi wolungama, osati chifukwa chotsatira chilamulo, koma chifukwa chokhulupirira+ Yesu Khristu basi.+ Choncho ifeyo tikukhulupirira Khristu Yesu kuti tionedwe olungama chifukwa chokhulupirira Khristu, osati chifukwa chotsatira chilamulo. Tachita zimenezi chifukwa palibe munthu amene amaonedwa wolungama chifukwa chotsatira chilamulo.+

  • Aheberi 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Popeza Chilamulo chimangochitira chithunzi+ zinthu zabwino zimene zikubwera+ ndipo si zinthu zenizenizo, sichingachititse* amene amalambira Mulungu kukhala angwiro pogwiritsa ntchito nsembe zimene amapereka mosalekeza chaka chilichonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena