Yohane 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine njira,+ choonadi+ ndi moyo.+ Palibe amene amafika kwa Atate osadzera mwa ine.+ Aheberi 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho, tiyeni tizifika kumpando wachifumu wa Mulungu ndipo tizipemphera ndi ufulu wa kulankhula+ kuti atichitire chifundo komanso kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu pa nthawi yoyenera.
6 Yesu anamuuza kuti: “Ine ndine njira,+ choonadi+ ndi moyo.+ Palibe amene amafika kwa Atate osadzera mwa ine.+
16 Choncho, tiyeni tizifika kumpando wachifumu wa Mulungu ndipo tizipemphera ndi ufulu wa kulankhula+ kuti atichitire chifundo komanso kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu pa nthawi yoyenera.