Yohane 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moyo unakhalapo kudzera mwa iye ndipo moyowo unali kuwala kounikira anthu.+ Yohane 6:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Mzimu ndi umene umapatsa moyo+ koma mnofu ulibe ntchito iliyonse. Mawu amene ndakuuzaniwa ndi mzimu ndiponso ndi moyo.+ Yohane 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Moyo wosatha adzaupeza+ akamaphunzira ndi kudziwa za inu, Mulungu yekhayo amene ndi woona,+ komanso za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+ Aroma 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+
63 Mzimu ndi umene umapatsa moyo+ koma mnofu ulibe ntchito iliyonse. Mawu amene ndakuuzaniwa ndi mzimu ndiponso ndi moyo.+
3 Moyo wosatha adzaupeza+ akamaphunzira ndi kudziwa za inu, Mulungu yekhayo amene ndi woona,+ komanso za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+
23 Chifukwa malipiro a uchimo ndi imfa,+ koma mphatso imene Mulungu amapereka ndi moyo wosatha+ kudzera mwa Khristu Yesu Ambuye wathu.+