Aheberi 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti Chilamulo sichinapangitse chilichonse kukhala changwiro,+ koma chiyembekezo+ chabwino kwambiri chimene anabweretsa kuwonjezera pa Chilamulocho, chinachita zimenezo. Ife tikuyandikira kwa Mulungu chifukwa cha chiyembekezo chimenecho.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2023, tsa. 25
19 Pakuti Chilamulo sichinapangitse chilichonse kukhala changwiro,+ koma chiyembekezo+ chabwino kwambiri chimene anabweretsa kuwonjezera pa Chilamulocho, chinachita zimenezo. Ife tikuyandikira kwa Mulungu chifukwa cha chiyembekezo chimenecho.+