Salimo 143:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musandiimbe mlandu ine mtumiki wanu,+Pakuti palibe aliyense wamoyo amene angakhale wolungama pamaso panu.+ Machitidwe 13:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Dziwaninso kuti pa zinthu zonse zimene kunali kosatheka kuti muyesedwe opanda mlandu kudzera m’chilamulo cha Mose,+ aliyense wokhulupirira akuyesedwa wopanda mlandu kudzera mwa Iyeyu.+ Aroma 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndani adzasumira mlandu anthu a Mulungu ochita kusankhidwa?+ Mulungu ndiye amawayesa olungama.+
2 Musandiimbe mlandu ine mtumiki wanu,+Pakuti palibe aliyense wamoyo amene angakhale wolungama pamaso panu.+
39 Dziwaninso kuti pa zinthu zonse zimene kunali kosatheka kuti muyesedwe opanda mlandu kudzera m’chilamulo cha Mose,+ aliyense wokhulupirira akuyesedwa wopanda mlandu kudzera mwa Iyeyu.+