Yesaya 50:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene adzanene kuti ndine wolungama ali pafupi.+ Ndani angalimbane nane? Tiyeni tikaonane pabwalo lamilandu.+ Kodi wotsutsana nane pa mlandu ndani?+ Abwere kufupi.+ Akolose 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 tsopano wagwirizana+ nanunso pogwiritsa ntchito thupi lanyama la mwanayo kudzera mu imfa yake.+ Wachita izi kuti akuperekeni pamaso pa iyeyo, muli opatulika ndi opanda chilema,+ ndiponso opanda chifukwa chokunenezerani.+
8 Amene adzanene kuti ndine wolungama ali pafupi.+ Ndani angalimbane nane? Tiyeni tikaonane pabwalo lamilandu.+ Kodi wotsutsana nane pa mlandu ndani?+ Abwere kufupi.+
22 tsopano wagwirizana+ nanunso pogwiritsa ntchito thupi lanyama la mwanayo kudzera mu imfa yake.+ Wachita izi kuti akuperekeni pamaso pa iyeyo, muli opatulika ndi opanda chilema,+ ndiponso opanda chifukwa chokunenezerani.+