Yesaya 41:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Zilumba inu,+ mvetserani mawu anga mutakhala chete, ndipo mitundu ya anthu+ ipezenso mphamvu. Ibwere pafupi,+ kenako ilankhule. Anthu inu bwerani kufupi nane kumalo oweruzira mlandu.+
41 “Zilumba inu,+ mvetserani mawu anga mutakhala chete, ndipo mitundu ya anthu+ ipezenso mphamvu. Ibwere pafupi,+ kenako ilankhule. Anthu inu bwerani kufupi nane kumalo oweruzira mlandu.+