Mika 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu imvani zimene Yehova akunena.+ Nyamukani mukanene mlandu wanu kwa mapiri ndipo zitunda zikamve mawu anu.+
6 Anthu inu imvani zimene Yehova akunena.+ Nyamukani mukanene mlandu wanu kwa mapiri ndipo zitunda zikamve mawu anu.+