Salimo 50:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akuitana kumwamba ndi dziko lapansi+Kuti apereke chiweruzo kwa anthu ake. Iye akuti:+ Yesaya 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Tsopano inu anthu okhala mu Yerusalemu ndiponso inu amuna a mu Yuda, weruzani pakati pa ine ndi munda wanga wa mpesa.+ Ezekieli 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “Koma iwe mwana wa munthu, losera zokhudza mapiri a ku Isiraeli. Unene kuti, ‘Inu mapiri a ku Isiraeli,+ tamverani mawu a Yehova.
3 “Tsopano inu anthu okhala mu Yerusalemu ndiponso inu amuna a mu Yuda, weruzani pakati pa ine ndi munda wanga wa mpesa.+
36 “Koma iwe mwana wa munthu, losera zokhudza mapiri a ku Isiraeli. Unene kuti, ‘Inu mapiri a ku Isiraeli,+ tamverani mawu a Yehova.