Deuteronomo 4:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anakuchititsani kumva mawu ake kuchokera kumwamba n’cholinga chakuti akulangizeni kuti muzimumvera. Padziko lapansi pano, iye anakuchititsani kuona moto wake woopsa, ndipo munamva mawu ake kuchokera pakati pa moto.+ Deuteronomo 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndaika moyo ndi imfa, dalitso+ ndi temberero+ pamaso panu.+ Kumwamba ndi dziko lapansi ndi mboni pa zochita zanu.+ Choncho inuyo ndi mbadwa zanu+ musankhe moyo kuti mukhalebe ndi moyo.+ Deuteronomo 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Tamverani kumwamba inu, ndiloleni ndilankhule.Ndipo dziko lapansi limve mawu a pakamwa panga.+ Yesaya 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani+ kumwamba inu, ndipo tchera khutu iwe dziko lapansi, chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana ndi kuwakulitsa,+ koma iwo andipandukira.+
36 Anakuchititsani kumva mawu ake kuchokera kumwamba n’cholinga chakuti akulangizeni kuti muzimumvera. Padziko lapansi pano, iye anakuchititsani kuona moto wake woopsa, ndipo munamva mawu ake kuchokera pakati pa moto.+
19 Ndaika moyo ndi imfa, dalitso+ ndi temberero+ pamaso panu.+ Kumwamba ndi dziko lapansi ndi mboni pa zochita zanu.+ Choncho inuyo ndi mbadwa zanu+ musankhe moyo kuti mukhalebe ndi moyo.+
2 Imvani+ kumwamba inu, ndipo tchera khutu iwe dziko lapansi, chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana ndi kuwakulitsa,+ koma iwo andipandukira.+