Yeremiya 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Tamverani anthu inu. Tcherani khutu. Musadzikweze+ pakuti Yehova ndi amene wanena zimenezi.+ Aheberi 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Kalekale, Mulungu analankhula ndi makolo athu nthawi zambiri+ ndiponso m’njira zambiri kudzera mwa aneneri.+
1 Kalekale, Mulungu analankhula ndi makolo athu nthawi zambiri+ ndiponso m’njira zambiri kudzera mwa aneneri.+