Ekisodo 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu ndi kuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Pamenepo anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+ Yeremiya 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 kuchokera tsiku limene makolo anu anatuluka m’dziko la Iguputo kufikira lero.+ Ndinapitiriza kukutumizirani atumiki anga onse aneneri, tsiku ndi tsiku ndinali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza.+ Ezekieli 33:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma mawu ako akadzakwaniritsidwa, pakuti adzakwaniritsidwa ndithu,+ iwo adzadziwa kuti pakati pawo panalidi mneneri.”+ Luka 1:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 monga mmene iye ananenera kudzera pakamwa pa aneneri ake oyera akale,+ Machitidwe 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ameneyu kumwamba kuyenera kumusunga+ mpaka nthawi za kubwezeretsa+ zinthu zonse, kumene Mulungu ananena kudzera mwa aneneri ake oyera+ akale.
3 Ndiyeno Mose anapita kwa anthu ndi kuwafotokozera mawu onse a Yehova ndi zigamulo zake zonse.+ Pamenepo anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Mawu onse amene Yehova wanena tidzachita.”+
25 kuchokera tsiku limene makolo anu anatuluka m’dziko la Iguputo kufikira lero.+ Ndinapitiriza kukutumizirani atumiki anga onse aneneri, tsiku ndi tsiku ndinali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza.+
33 Koma mawu ako akadzakwaniritsidwa, pakuti adzakwaniritsidwa ndithu,+ iwo adzadziwa kuti pakati pawo panalidi mneneri.”+
21 Ameneyu kumwamba kuyenera kumusunga+ mpaka nthawi za kubwezeretsa+ zinthu zonse, kumene Mulungu ananena kudzera mwa aneneri ake oyera+ akale.