Aroma 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti ngati pamene tinali adani,+ tinayanjanitsidwa kwa Mulungu kudzera mu imfa ya Mwana wake,+ nanji tsopano pamene tayanjanitsidwa, tidzapulumutsidwa ndithu ndi moyo wake.+ Aefeso 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiponso kuti kudzera mwa mtengo wozunzikirapo*+ ayanjanitse+ magulu awiri a anthuwo kwa Mulungu, ndipo anthuwo akhale thupi limodzi,+ chifukwa anali atapheratu chidanicho+ kudzera mwa iye mwini.
10 Pakuti ngati pamene tinali adani,+ tinayanjanitsidwa kwa Mulungu kudzera mu imfa ya Mwana wake,+ nanji tsopano pamene tayanjanitsidwa, tidzapulumutsidwa ndithu ndi moyo wake.+
16 Ndiponso kuti kudzera mwa mtengo wozunzikirapo*+ ayanjanitse+ magulu awiri a anthuwo kwa Mulungu, ndipo anthuwo akhale thupi limodzi,+ chifukwa anali atapheratu chidanicho+ kudzera mwa iye mwini.