Aroma 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngati tinagwirizanitsidwa ndi Mulungu kudzera mu imfa ya Mwana wake+ pa nthawi imene tinali adani, ndiye kuti tidzapulumutsidwa ndithu ndi moyo wake, popeza panopa tagwirizanitsidwa.
10 Ngati tinagwirizanitsidwa ndi Mulungu kudzera mu imfa ya Mwana wake+ pa nthawi imene tinali adani, ndiye kuti tidzapulumutsidwa ndithu ndi moyo wake, popeza panopa tagwirizanitsidwa.