2 Akorinto 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma zinthu zonse n’zochokera kwa Mulungu, amene anatigwirizanitsa+ ndi iyeyo kudzera mwa Khristu, ndipo anatipatsa utumiki+ wokhazikitsanso mtendere. Akolose 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 tsopano wagwirizana+ nanunso pogwiritsa ntchito thupi lanyama la mwanayo kudzera mu imfa yake.+ Wachita izi kuti akuperekeni pamaso pa iyeyo, muli opatulika ndi opanda chilema,+ ndiponso opanda chifukwa chokunenezerani.+
18 Koma zinthu zonse n’zochokera kwa Mulungu, amene anatigwirizanitsa+ ndi iyeyo kudzera mwa Khristu, ndipo anatipatsa utumiki+ wokhazikitsanso mtendere.
22 tsopano wagwirizana+ nanunso pogwiritsa ntchito thupi lanyama la mwanayo kudzera mu imfa yake.+ Wachita izi kuti akuperekeni pamaso pa iyeyo, muli opatulika ndi opanda chilema,+ ndiponso opanda chifukwa chokunenezerani.+