Aroma 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu anatsutsa uchimo mwa kugwiritsa ntchito thupi potumiza Mwana wake+ m’thupi lofanana ndi lauchimo+ kuti athane ndi uchimo.+ Pakuti Chilamulo sichinathe kuchita zimenezi+ pokhala chofooka+ chifukwa cha thupi. Aheberi 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti Chilamulo sichinapangitse chilichonse kukhala changwiro,+ koma chiyembekezo+ chabwino kwambiri chimene anabweretsa kuwonjezera pa Chilamulocho, chinachita zimenezo. Ife tikuyandikira kwa Mulungu chifukwa cha chiyembekezo chimenecho.+ Aheberi 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Popeza Chilamulo ndicho mthunzi chabe+ wa zinthu zabwino zimene zikubwera osati zinthu zenizenizo, ndiye kuti anthu wamba sangachititse anthu amene amalambira Mulungu kukhala angwiro. Iwo sangathe kuchita zimenezi mwa nsembe zimodzimodzizo zimene amapereka mosalekeza chaka ndi chaka.+
3 Mulungu anatsutsa uchimo mwa kugwiritsa ntchito thupi potumiza Mwana wake+ m’thupi lofanana ndi lauchimo+ kuti athane ndi uchimo.+ Pakuti Chilamulo sichinathe kuchita zimenezi+ pokhala chofooka+ chifukwa cha thupi.
19 Pakuti Chilamulo sichinapangitse chilichonse kukhala changwiro,+ koma chiyembekezo+ chabwino kwambiri chimene anabweretsa kuwonjezera pa Chilamulocho, chinachita zimenezo. Ife tikuyandikira kwa Mulungu chifukwa cha chiyembekezo chimenecho.+
10 Popeza Chilamulo ndicho mthunzi chabe+ wa zinthu zabwino zimene zikubwera osati zinthu zenizenizo, ndiye kuti anthu wamba sangachititse anthu amene amalambira Mulungu kukhala angwiro. Iwo sangathe kuchita zimenezi mwa nsembe zimodzimodzizo zimene amapereka mosalekeza chaka ndi chaka.+