Mateyu 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 asalemekeze bambo ake.’+ Chotero mwasandutsa mawu a Mulungu kukhala opanda pake chifukwa cha miyambo yanu.+ Luka 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma Afarisi ndi anthu odziwa Chilamulo ananyalanyaza malangizo+ amene Mulungu anawapatsa. Choncho Yohane sanawabatize.)
6 asalemekeze bambo ake.’+ Chotero mwasandutsa mawu a Mulungu kukhala opanda pake chifukwa cha miyambo yanu.+
30 Koma Afarisi ndi anthu odziwa Chilamulo ananyalanyaza malangizo+ amene Mulungu anawapatsa. Choncho Yohane sanawabatize.)