Maliko 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwa kuchita zimenezi, mumapangitsa mawu a Mulungu+ kukhala opanda pake chifukwa cha mwambo wanu umene munaupereka kwa anthu. Ndipo mumachita zinthu zambiri+ zofanana ndi zimenezi.”
13 Mwa kuchita zimenezi, mumapangitsa mawu a Mulungu+ kukhala opanda pake chifukwa cha mwambo wanu umene munaupereka kwa anthu. Ndipo mumachita zinthu zambiri+ zofanana ndi zimenezi.”