Mateyu 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 asalemekeze bambo ake.’+ Chotero mwasandutsa mawu a Mulungu kukhala opanda pake chifukwa cha miyambo yanu.+
6 asalemekeze bambo ake.’+ Chotero mwasandutsa mawu a Mulungu kukhala opanda pake chifukwa cha miyambo yanu.+