2 Samueli 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova andibwezere mogwirizana ndi chilungamo changa,+Andibwezere mogwirizana ndi kukhala kwanga woyera pamaso pake.+ Miyambo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti njira za munthu zili pamaso pa Yehova,+ ndipo iye amaonetsetsa njira zake zonse.+
25 Yehova andibwezere mogwirizana ndi chilungamo changa,+Andibwezere mogwirizana ndi kukhala kwanga woyera pamaso pake.+