Salimo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwasanthula mtima wanga, mwandifufuza usiku,+Ndipo mwandiyenga. Mudzaona kuti sindinaganizire kuchita choipa chilichonse.+Pakamwa panga sipadzaphwanya malamulo.+ Yeremiya 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti maso anga akuona njira zawo zonse. Anthuwo sanabisike kwa ine, ndipo zolakwa zawo sizinabisike pamaso panga.+ Aheberi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+
3 Mwasanthula mtima wanga, mwandifufuza usiku,+Ndipo mwandiyenga. Mudzaona kuti sindinaganizire kuchita choipa chilichonse.+Pakamwa panga sipadzaphwanya malamulo.+
17 Pakuti maso anga akuona njira zawo zonse. Anthuwo sanabisike kwa ine, ndipo zolakwa zawo sizinabisike pamaso panga.+
13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino. Ndipotu ife tikuyenera kudzayankha pa zochita zathu kwa Mulungu amene amaona zonseyo.+