Salimo 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova amasanthula anthu olungama ndi oipa omwe,+Ndipo Mulungu amadana kwambiri ndi aliyense wokonda chiwawa.+ Salimo 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzatamanda Yehova amene wandipatsa malangizo.+Ndithudi, usiku impso zanga zandiwongolera.+ 1 Akorinto 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti sindikudziwa+ kanthu kalikonse konditsutsa mumtima mwanga. Koma zimenezi sizikutanthauza kuti basi ndine wolungama, koma Yehova ndiye amandifufuza.+
5 Yehova amasanthula anthu olungama ndi oipa omwe,+Ndipo Mulungu amadana kwambiri ndi aliyense wokonda chiwawa.+
4 Pakuti sindikudziwa+ kanthu kalikonse konditsutsa mumtima mwanga. Koma zimenezi sizikutanthauza kuti basi ndine wolungama, koma Yehova ndiye amandifufuza.+