Genesis 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo, Yehova anaona kuti kuipa kwa anthu kwachuluka padziko lapansi, ndipo malingaliro+ onse a m’mitima ya anthu anali oipa okhaokha nthawi zonse.+ Genesis 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pambuyo pake Yehova anauza Nowa kuti: “Lowa m’chingalawacho, iwe ndi banja lako,+ chifukwa iwe ndi amene ndakuona kuti ndiwe wolungama pakati pa m’badwo uwu.+ Genesis 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano zimenezi zitapita, Mulungu woona anamuyesa Abulahamu+ pomuuza kuti: “Abulahamu!” Iye anayankha kuti: “Ine mbuyanga!”+
5 Pamenepo, Yehova anaona kuti kuipa kwa anthu kwachuluka padziko lapansi, ndipo malingaliro+ onse a m’mitima ya anthu anali oipa okhaokha nthawi zonse.+
7 Pambuyo pake Yehova anauza Nowa kuti: “Lowa m’chingalawacho, iwe ndi banja lako,+ chifukwa iwe ndi amene ndakuona kuti ndiwe wolungama pakati pa m’badwo uwu.+
22 Tsopano zimenezi zitapita, Mulungu woona anamuyesa Abulahamu+ pomuuza kuti: “Abulahamu!” Iye anayankha kuti: “Ine mbuyanga!”+