Yesaya 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako ndinayamba kumva mawu a Yehova akufunsa kuti: “Kodi nditumiza ndani, ndipo ndani apite m’malo mwa ife?”+ Ine ndinayankha kuti: “Ine ndilipo! Nditumizeni.”+
8 Kenako ndinayamba kumva mawu a Yehova akufunsa kuti: “Kodi nditumiza ndani, ndipo ndani apite m’malo mwa ife?”+ Ine ndinayankha kuti: “Ine ndilipo! Nditumizeni.”+