Miyambo 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Usasirire munthu wachiwawa,+ kapena kusankha njira zake.+ Miyambo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Maso odzikweza,+ lilime lonama,+ manja okhetsa magazi a anthu osalakwa,+