Yobu 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndagwira chilungamo changa ndipo sindichitaya.+Mtima wanga sudzandinyoza masiku anga onse.+ Machitidwe 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene anali kuyang’anitsitsa Khoti Lalikulu la Ayudalo, Paulo anati: “Amuna inu, abale anga, ndachita zinthu popanda chikumbumtima changa kunditsutsa ngakhale pang’ono pamaso pa Mulungu+ mpaka lero.” Machitidwe 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pambali imeneyi, ndikuyesetsa mwakhama, kuchita mozindikira+ kuti ndisapalamule kwa Mulungu kapena kwa anthu.
23 Pamene anali kuyang’anitsitsa Khoti Lalikulu la Ayudalo, Paulo anati: “Amuna inu, abale anga, ndachita zinthu popanda chikumbumtima changa kunditsutsa ngakhale pang’ono pamaso pa Mulungu+ mpaka lero.”
16 Pambali imeneyi, ndikuyesetsa mwakhama, kuchita mozindikira+ kuti ndisapalamule kwa Mulungu kapena kwa anthu.