-
Yeremiya 42:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ife tikukutuma kwa Yehova Mulungu wathu, kaya mawu ake ndi otikomera kapena otiipira, tidzamverabe mawuwo. Tidzachita zimenezi kuti zinthu zitiyendere bwino chifukwa chomvera mawu a Yehova Mulungu wathu.”
-