Yeremiya 42:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kaya mawu a Yehova Mulungu wathu ndi otikomera kapena otiipira, ife tidzamvera mawuwo. Tidzatero kuti zinthu zitiyendere bwino chifukwa chomvera mawu a Yehova Mulungu wathu.”+
6 Kaya mawu a Yehova Mulungu wathu ndi otikomera kapena otiipira, ife tidzamvera mawuwo. Tidzatero kuti zinthu zitiyendere bwino chifukwa chomvera mawu a Yehova Mulungu wathu.”+