Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Usasiye kukoma mtima kosatha ndi choonadi.+ Uzimange m’khosi mwako+ ndiponso uzilembe pamtima pako.+

  • Miyambo 19:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Chinthu chosiririka mwa munthu wochokera kufumbi ndicho kukoma mtima kwake kosatha,+ ndipo munthu wosauka ali bwino kuposa munthu wonama.+

  • Hoseya 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti ndimakondwera ndi kukoma mtima kosatha,+ osati ndi nsembe.+ Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati ndi nsembe zopsereza zathunthu.+

  • Zekariya 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Muzichita chilungamo chenicheni poweruza milandu.+ Muzisonyezana kukoma mtima kosatha+ ndi chifundo.+

  • Aefeso 4:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Koma khalani okomerana mtima,+ achifundo chachikulu,+ okhululukirana ndi mtima wonse, monga mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+

  • Akolose 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chotero monga ochita kusankhidwa ndi Mulungu,+ oyera ndi okondedwa, valani chifundo+ chachikulu, kukoma mtima, kudzichepetsa,+ kufatsa,+ ndi kuleza mtima.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena