Maliko 12:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndiyeno anakhala pansi moyang’anana ndi moponyamo zopereka+ ndipo anali kuona mmene khamu la anthu linali kuponyera ndalama moponya zoperekamo. Anthu ambiri olemera anali kuponyamo makobidi ambiri.+ 2 Akorinto 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene iwo anali kuyesedwa kwambiri chifukwa cha mavuto, anali achimwemwe kwambiri ndiponso anasonyeza kuwolowa manja kwakukulu, ndipo anachita zimenezi ngakhale kuti anali pa umphawi wadzaoneni.+
41 Ndiyeno anakhala pansi moyang’anana ndi moponyamo zopereka+ ndipo anali kuona mmene khamu la anthu linali kuponyera ndalama moponya zoperekamo. Anthu ambiri olemera anali kuponyamo makobidi ambiri.+
2 Pamene iwo anali kuyesedwa kwambiri chifukwa cha mavuto, anali achimwemwe kwambiri ndiponso anasonyeza kuwolowa manja kwakukulu, ndipo anachita zimenezi ngakhale kuti anali pa umphawi wadzaoneni.+