Yesaya 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Taonani! Mzinda wokhulupirika uja+ wasanduka hule.+ Unali wodzaza ndi chilungamo+ ndipo zachilungamo zinali kukhala mwa iye,+ koma tsopano muli zigawenga zopha anthu.+ Yesaya 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 N’chiyaninso chimene ndingachite m’munda wanga wa mpesawu chimene sindinachitemo kale?+ Ine ndinali kuyembekezera kuti ubereka mphesa zabwino, koma n’chifukwa chiyani unabereka mphesa zam’tchire?
21 Taonani! Mzinda wokhulupirika uja+ wasanduka hule.+ Unali wodzaza ndi chilungamo+ ndipo zachilungamo zinali kukhala mwa iye,+ koma tsopano muli zigawenga zopha anthu.+
4 N’chiyaninso chimene ndingachite m’munda wanga wa mpesawu chimene sindinachitemo kale?+ Ine ndinali kuyembekezera kuti ubereka mphesa zabwino, koma n’chifukwa chiyani unabereka mphesa zam’tchire?