Salimo 80:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munachititsa mtengo wa mpesa kuchoka mu Iguputo.+Munapitikitsa mitundu ya anthu kuti mubzalemo mtengowo.+ Yeremiya 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Abusa ambiri+ awononga munda wanga wa mpesa.+ Apondaponda cholowa changa.+ Cholowa changa chosiririka+ achisandutsa bwinja moti palibe aliyense amene akukhalamo. Luka 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno iye anayamba kuuza anthuwo fanizo ili: “Munthu wina analima munda wa mpesa,+ ndipo anasiya mundawo m’manja mwa alimi n’kupita kudziko lina kumene anakhalako nthawi yaitali ndithu.+
8 Munachititsa mtengo wa mpesa kuchoka mu Iguputo.+Munapitikitsa mitundu ya anthu kuti mubzalemo mtengowo.+
10 Abusa ambiri+ awononga munda wanga wa mpesa.+ Apondaponda cholowa changa.+ Cholowa changa chosiririka+ achisandutsa bwinja moti palibe aliyense amene akukhalamo.
9 Ndiyeno iye anayamba kuuza anthuwo fanizo ili: “Munthu wina analima munda wa mpesa,+ ndipo anasiya mundawo m’manja mwa alimi n’kupita kudziko lina kumene anakhalako nthawi yaitali ndithu.+