-
1 Akorinto 12:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Sikuti onse angakhale atumwi, angatero ngati? Sikuti onse angakhale aneneri, angatero ngati? Sikuti onse angakhale aphunzitsi, angatero ngati? Si onse amachita ntchito zamphamvu, ndi onse ngati?
-