Ekisodo 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Usapondereze mlendo wokhala pakati panu,+ popeza mukudziwa mmene zimakhalira ukakhala mlendo, chifukwa inunso munali alendo m’dziko la Iguputo.+
9 “Usapondereze mlendo wokhala pakati panu,+ popeza mukudziwa mmene zimakhalira ukakhala mlendo, chifukwa inunso munali alendo m’dziko la Iguputo.+