Salimo 62:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,+Ndipo musakhale wachabechabe chifukwa chochita uchifwamba.+Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu wonse usakhale pachumacho.+ Yesaya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova adzaweruza achikulire pakati pa anthu ake ndi akalonga ake.+ “Inuyo mwatentha munda wa mpesa. Zinthu zimene zinabedwa kwa anthu ovutika zili m’nyumba zanu.+
10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,+Ndipo musakhale wachabechabe chifukwa chochita uchifwamba.+Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu wonse usakhale pachumacho.+
14 Yehova adzaweruza achikulire pakati pa anthu ake ndi akalonga ake.+ “Inuyo mwatentha munda wa mpesa. Zinthu zimene zinabedwa kwa anthu ovutika zili m’nyumba zanu.+