Yesaya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova adzaweruza akulu komanso akalonga a anthu ake. “Inuyo mwawotcha munda wa mpesa,Ndipo zinthu zimene munaba kwa anthu osauka zili mʼnyumba zanu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Yesaya 1, tsa. 58
14 Yehova adzaweruza akulu komanso akalonga a anthu ake. “Inuyo mwawotcha munda wa mpesa,Ndipo zinthu zimene munaba kwa anthu osauka zili mʼnyumba zanu.+