Yesaya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova adzaweruza achikulire pakati pa anthu ake ndi akalonga ake.+ “Inuyo mwatentha munda wa mpesa. Zinthu zimene zinabedwa kwa anthu ovutika zili m’nyumba zanu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Yesaya 1, tsa. 58
14 Yehova adzaweruza achikulire pakati pa anthu ake ndi akalonga ake.+ “Inuyo mwatentha munda wa mpesa. Zinthu zimene zinabedwa kwa anthu ovutika zili m’nyumba zanu.+