Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ‘Ndithudi, maso ako ndi mtima wako sizikulakalaka china chilichonse koma phindu lachinyengo,+ anthu osalakwa kuti ukhetse magazi awo+ komanso kuba mwachinyengo ndi kulanda.’

  • Ezekieli 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 ngati amazunza munthu wosautsika ndi wosauka,+ ngati amalanda zinthu za ena mwauchifwamba,+ ngati sabweza chikole,+ ngati amakweza maso ake kuyang’ana mafano onyansa,+ ndiye kuti wachita chinthu chonyansa.+

  • Ezekieli 22:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anthu alandira ziphuphu kuti akhetse magazi.+ Iwe walandira chiwongoladzanja+ ndi kuchita katapira.+ Ukupeza phindu losayenera mwa kubera anzako+ mwachinyengo+ ndipo ine wandiiwala,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena