Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 7:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Nditaona+ chovala chamtengo wapatali cha ku Sinara,+ pakati pa katundu wotsalayo, chokongola m’maonekedwe, komanso masekeli* a siliva 200, ndi mtanda umodzi wa golide wolemera masekeli 50, ndinazikhumba zinthuzo,+ ndipo ndinazitenga.+ Panopo chovalacho ndinachikumbira pansi, pakati pa hema wanga, pamodzi ndi ndalamazo, ndipo ndalamazo zili pansi pa chovalacho.”+

  • Salimo 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pakuti woipa amadzitamandira ndi zilakolako zake zadyera,+

      Ndipo wopanga phindu lachinyengo+ amadzitamanda.

      נ [Nun]

      Iye amanyoza Yehova.+

  • Salimo 119:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  37 Chititsani maso anga kuti asaone zinthu zopanda pake.+

      Ndiyendetseni m’njira yanu kuti ndikhalebe wamoyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena