Yesaya 57:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Ine ndinakwiya chifukwa cha phindu lachinyengo limene analipeza mosayenera.+ Ndinakwiya ndipo ndinamulanga. Ndinabisa nkhope yanga chifukwa cha mkwiyo.+ Koma iye ankangoyendabe ngati wopanduka+ m’njira ya mtima wake. Maliko 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi mwinimunda wa mpesawo adzachita chiyani? Adzabwera ndi kupha alimiwo, ndipo munda wa mpesawo+ adzaupereka kwa ena.+ Luka 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atatero anamutulutsa+ m’munda wa mpesawo ndi kumupha.+ Pamenepa, kodi mwini munda wa mpesa uja adzachita chiyani kwa alimiwo?+
17 “Ine ndinakwiya chifukwa cha phindu lachinyengo limene analipeza mosayenera.+ Ndinakwiya ndipo ndinamulanga. Ndinabisa nkhope yanga chifukwa cha mkwiyo.+ Koma iye ankangoyendabe ngati wopanduka+ m’njira ya mtima wake.
9 Kodi mwinimunda wa mpesawo adzachita chiyani? Adzabwera ndi kupha alimiwo, ndipo munda wa mpesawo+ adzaupereka kwa ena.+
15 Atatero anamutulutsa+ m’munda wa mpesawo ndi kumupha.+ Pamenepa, kodi mwini munda wa mpesa uja adzachita chiyani kwa alimiwo?+