Mateyu 21:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Iwo anayankha kuti: “Chifukwa chakuti ndi oipa, adzawawononga koopsa+ ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa alimi ena, amene angam’patse zipatso m’nyengo yake.”+ Luka 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adzabwera ndi kupha alimiwo ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa ena.”+ Atamva zimenezi iwo anati: “Ayi zisatero ndithu!”
41 Iwo anayankha kuti: “Chifukwa chakuti ndi oipa, adzawawononga koopsa+ ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa alimi ena, amene angam’patse zipatso m’nyengo yake.”+
16 Adzabwera ndi kupha alimiwo ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa ena.”+ Atamva zimenezi iwo anati: “Ayi zisatero ndithu!”