Zekariya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yerusalemu+ ndidzamusandutsa mbale yolowa yochititsa mitundu yonse ya anthu omuzungulira kuyenda dzandidzandi.+ Mdani adzazungulira Yuda, adzazungulira Yerusalemu.+
2 “Yerusalemu+ ndidzamusandutsa mbale yolowa yochititsa mitundu yonse ya anthu omuzungulira kuyenda dzandidzandi.+ Mdani adzazungulira Yuda, adzazungulira Yerusalemu.+