Maliko 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi mwinimunda wa mpesawo adzachita chiyani? Adzabwera ndi kupha alimiwo, ndipo munda wa mpesawo+ adzaupereka kwa ena.+ Luka 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adzabwera ndi kupha alimiwo ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa ena.”+ Atamva zimenezi iwo anati: “Ayi zisatero ndithu!” Machitidwe 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwo atapitiriza kumutsutsa ndi kulankhula monyoza,+ iye anakutumula zovala zake+ ndi kuwauza kuti: “Magazi anu+ akhale pamitu panu. Ine ndilibe mlandu.+ Kuyambira tsopano ndizipita kwa anthu a mitundu ina.”+
9 Kodi mwinimunda wa mpesawo adzachita chiyani? Adzabwera ndi kupha alimiwo, ndipo munda wa mpesawo+ adzaupereka kwa ena.+
16 Adzabwera ndi kupha alimiwo ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa ena.”+ Atamva zimenezi iwo anati: “Ayi zisatero ndithu!”
6 Koma iwo atapitiriza kumutsutsa ndi kulankhula monyoza,+ iye anakutumula zovala zake+ ndi kuwauza kuti: “Magazi anu+ akhale pamitu panu. Ine ndilibe mlandu.+ Kuyambira tsopano ndizipita kwa anthu a mitundu ina.”+