Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Mdaniyo anati, ‘Ndiwathamangira,+ ndi kuwapeza!+

      Ndigawa chuma chawo.+ Pamenepo moyo wanga ukhutira ndi zimene ndawachita!

      Ndisolola lupanga langa! Dzanja langa liwawononga!’+

  • Salimo 94:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Iwo amalankhula zopanda pake, ndipo amalankhula mosasamala.+

      Onse ochita zopweteka anzawo amadzitukumula.+

  • Salimo 106:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anasonyeza chikhumbo chawo chadyera m’chipululu,+

      Ndipo anayesa Mulungu m’chipululumo.+

  • Hoseya 12:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Efuraimu akupitiriza kunena kuti, ‘Inetu ndalemeradi,+ ndapeza zinthu zamtengo wapatali.+ Palibe amene angapeze cholakwa chachikulu pa ntchito zanga zonse.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena