Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 17:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno anthu anayamba kukangana ndi Mose kuti:+ “Tipatse madzi timwe.” Koma Mose anawafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukukangana ndi ine? N’chifukwa chiyani mukupitiriza kuyesa Yehova?”+

  • Numeri 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma anthu onse amene aona ulemerero wanga,+ ndi zizindikiro zanga+ zimene ndinachita ku Iguputo, ndi zimene ndachita m’chipululu, amene akupitirizabe kundiyesa+ maulendo 10 onsewa, amenenso sanamvere mawu anga,+

  • Salimo 78:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Iwo anapitiriza kuyesa Mulungu m’mitima yawo+

      Mwa kupempha chakudya china chimene mtima wawo unalakalaka.+

  • 1 Akorinto 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kapena tisamuyese Yehova,+ mmene ena mwa iwo anamuyesera,+ n’kuwonongeka polumidwa ndi njoka.+

  • Aheberi 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 M’chipululumo, makolo anu anandiyesa ndi mayesero, ngakhale kuti anali ataona ntchito zanga+ kwa zaka 40.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena