Ekisodo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nthawi yomweyo iwo anati: “Yehova aone zimene mwachitazi ndipo akuweruzeni,+ chifukwa mwatinunkhitsa+ pamaso pa Farao ndi atumiki ake, moti mwawapatsa lupanga m’manja mwawo kuti atiphe.”+ Numeri 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana onse a Isiraeli anayamba kudandaula za Mose ndi Aroni.+ Ndipo khamu lonselo linati: “Zikanakhala bwino tikanangofera ku Iguputo, kapena tikanangofera m’chipululu muno. Numeri 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo anthuwo anayamba kukangana+ ndi Mose, kuti: “Zikanakhala bwino tikanangofera limodzi ndi abale athu amene anafa pamaso pa Yehova aja.+
21 Nthawi yomweyo iwo anati: “Yehova aone zimene mwachitazi ndipo akuweruzeni,+ chifukwa mwatinunkhitsa+ pamaso pa Farao ndi atumiki ake, moti mwawapatsa lupanga m’manja mwawo kuti atiphe.”+
2 Ana onse a Isiraeli anayamba kudandaula za Mose ndi Aroni.+ Ndipo khamu lonselo linati: “Zikanakhala bwino tikanangofera ku Iguputo, kapena tikanangofera m’chipululu muno.
3 Pamenepo anthuwo anayamba kukangana+ ndi Mose, kuti: “Zikanakhala bwino tikanangofera limodzi ndi abale athu amene anafa pamaso pa Yehova aja.+