Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 11:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndipotu ine sindinakuchimwire, koma iwe ukundilakwira pomenyana nane. Yehova amene ndi Woweruza,+ aweruze lero pakati pa ana a Isiraeli ndi ana a Amoni.’”

  • 1 Samueli 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Onse olimbana ndi Yehova adzagwidwa ndi mantha.+

      Motsutsana nawo, iye adzagunda ngati mabingu kumwamba.+

      Yehova mwiniwake adzaweruza dziko lonse lapansi,+

      Kuti apereke mphamvu kwa mfumu yake,+

      Ndi kuti akweze nyanga ya wodzozedwa wake.”+

  • Yesaya 33:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pakuti Yehova ndiye Woweruza wathu.+ Yehova ndiye Wotipatsa Malamulo.+ Yehova ndiye Mfumu yathu.+ Iye adzatipulumutsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena