Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+ Zefaniya 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova Mulungu wako ali pakati pa anthu ako ndipo adzakupulumutsa chifukwa ndi wamphamvu.+ Iye adzakondwera nawe.+ Adzakhala phee chifukwa chokhutira ndi chikondi chimene akukusonyeza, ndipo adzafuula mosangalala chifukwa chokondwera nawe.
2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
17 Yehova Mulungu wako ali pakati pa anthu ako ndipo adzakupulumutsa chifukwa ndi wamphamvu.+ Iye adzakondwera nawe.+ Adzakhala phee chifukwa chokhutira ndi chikondi chimene akukusonyeza, ndipo adzafuula mosangalala chifukwa chokondwera nawe.