Ekisodo 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Mose analankhula mawu amenewa kwa ana a Isiraeli, koma iwo sanamvere Mose chifukwa chokhumudwa ndiponso chifukwa cha ntchito yowawa ya ukapolo.+ Ekisodo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho anthu anamva ludzu pamenepo, ndipo anthuwo anapitiriza kung’ung’udzira Mose kuti: “N’chifukwa chiyani unatitulutsa mu Iguputo kuti udzatiphe ndi ludzu, ifeyo pamodzi ndi ana athu ndi ziweto zathu?”+
9 Kenako Mose analankhula mawu amenewa kwa ana a Isiraeli, koma iwo sanamvere Mose chifukwa chokhumudwa ndiponso chifukwa cha ntchito yowawa ya ukapolo.+
3 Choncho anthu anamva ludzu pamenepo, ndipo anthuwo anapitiriza kung’ung’udzira Mose kuti: “N’chifukwa chiyani unatitulutsa mu Iguputo kuti udzatiphe ndi ludzu, ifeyo pamodzi ndi ana athu ndi ziweto zathu?”+