Ekisodo 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’chipululumo khamu lonse la ana a Isiraeli linayamba kung’ung’udzira Mose ndi Aroni.+